Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 55:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti inu mudzaturuka ndi kukondwa, ndi kutsogozedwa ndi mtendere; mapiri ndi zitunda, zidzayimba zolimba pamaso panu, ndi mitengo yonse ya m'thengo idzaomba m'manja mwao.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 55

Onani Yesaya 55:12 nkhani