Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 54:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kumeneku kuli kwa Ine monga madzi a Nowa; pakuti monga ndinalumbira kuti madzi a Nowa sadzamizanso pa dziko lapansi, momwemo ndinalumbira kuti sindidzakukwiyira iwe, pena kukudzudzula.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 54

Onani Yesaya 54:9 nkhani