Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 54:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'kukwiya kwa kusefukira ndinakubisira nkhope yanga kamphindi; koma ndi kukoma mtima kwa cikhalire ndidzakucitira cifundo, ati Yehova Mombolo wako.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 54

Onani Yesaya 54:8 nkhani