Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 54:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe cida cosulidwira iwe cidzapindula; ndipo lilime lonse limene lidzakangana nawe m'ciweruzo udzalitsutsa. Ici ndi colowa ca atumiki a Yehova, ndi cilungamo cao cimene cifuma kwa Ine, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 54

Onani Yesaya 54:17 nkhani