Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 52:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ambuye Yehova atero, Anthu anga ananka ku Aigupto poyamba paja, kukakhala kumeneko; ndipo Asuri anawatsendereza popanda cifukwa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 52

Onani Yesaya 52:4 nkhani