Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo iye anakumba mcerenje kuzungulira kwete, natolatola miyala pamenepo naokapo mpesa wosankhika, namangapo pakati pace nsanja, nasema mopondera mphesa, nayembekeza kuti udzabala mphesa, koma unangobala mphesa zosadya.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:2 nkhani