Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musaope inu, musakhale ndi mantha; kodi ndinanena kwa iwe zakale, ndi kuzionetsa zimenezo, ndipo inu ndinu mboni zanga. Kodi popanda Ine aliponso Mulungu? Iai, palibe thanthwe; sindidziwa liri lonse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:8 nkhani