ndi kunena za Koresi, Iye ndiye mbusa wanga, ndipo adzacita zofuna zanga zonse; ndi kunena za Yerusalemu, Adzamangidwa; ndi kwa Kacisi, Maziko ako adzaikidwa.