Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe wina wokumbukira, kapena kudziwa, kapena kuzindikira, ndi kuti, Ndatentha mbali yina pamoto, inde ndaocanso mkate pamakala pace, ndakazinga nyama ndi kuidya; kodi ndicipange cotsala cace, cikhale conyansa? ndidzagwadira kodi tsinde la mtengo?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:19 nkhani