Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 43:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwe sunanditengere Ine zoweta zazing'ono za nsembe zopsereza zako; kapena kundilemekeza ndi nsembe zako. Sindinakutumikiritsa ndi nsembe zaufa, kapena kukutopetsa ndi zonunkhira.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:23 nkhani