Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 43:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ine ndidzacita cinthu catsopano; tsopano cidzaoneka; kodi simudzacidziwa? Ndidzakonzadi njira m'cipululu, ndi mitsinje m'zidalala.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:19 nkhani