Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 43:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu ndinu mboni zanga, ati Yehova, ndi mtumiki wanga, amene ndakusankha; kuti mundidziwe, ndi kundikhulupirira Ine, ndi kuzindikira, kuti Ine ndine; ndisanakhale Ine, panalibe Mulungu wolengedwa, ngakhale pambuyo panga sipadzakhala wina.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:10 nkhani