Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

iwe amene ndinakuwira iwe zolimba kucokera ku malekezero a dziko lapansi, ndi kukuitana iwe kucokera m'ngondya zace, ndipo ndinati kwa iwe, Ndiwe mtumiki wanga ndakusankha, sindinakutaya kunja;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:9 nkhani