Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cotero mmisiri wa mitengo analimbikitsa wosula golidi, ndi iye amene asalaza ndi nyundo anamlimbikitsa iye amene amenya posulira, nanena za kulumikiza ndi nthobvu, Kuti kwabwino; ndipo iye akhomera fanolo misomali kuti lisasunthike.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:7 nkhani