Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, iwo onse, nchito zao zikhala zopanda pace ndi zacabe; mafano ao osungunula ndiwo mphepo ndi masokonezo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:29 nkhani