Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Ndipo pamene ndayang'ana, palibe munthu; ngakhale mwa iwo, palibe phungu, amene angathe kuyankha mau, pamene ndiwafunsa.

29. Taona, iwo onse, nchito zao zikhala zopanda pace ndi zacabe; mafano ao osungunula ndiwo mphepo ndi masokonezo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41