Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani wachula ico ciyambire, kuti ife ticidziwe? ndi nthawi zakale, kuti ife tinene, Iye ali wolungama? inde, palibe wina amene achula, inde, palibe wina amene asonyeza, inde, palibe wina amene amvetsa mau anu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:26 nkhani