Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzagwetsa mitsinje pazitunda zoti se, ndi akasupe pakati pa zigwa; ndidzasandutsa cipululu, cikhale thamanda lamadzi, ndi mtunda wouma ukhale magwero a madzi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:18 nkhani