Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Khalani cete pamaso pa Ine, zisumbu inu, anthu atengenso mphamvu; ayandikire; pamenepo alankhule; tiyeni, tiyandikire pamodzi kuciweruziro.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:1 nkhani