Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 40:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwe amene utengera mau abwino ku Ziyoni, kwera iwe pamwamba pa phiri lalitari; iwe amene utengera mau abwino ku Yerusalemu, kweza mau ako ndi mphamvu, kwezetsa usaope, nena ku midzi ya Yuda, Taonani, Mulungu wanu!

Werengani mutu wathunthu Yesaya 40

Onani Yesaya 40:9 nkhani