Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 40:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, Ambuye Yehova adzadza ngati wamphamvu, ndipo mkono wace udzalamulira; taonani, mphoto yace iri ndi Iye, ndipo cobwezera cace ciri patsogolo pa Iye.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 40

Onani Yesaya 40:10 nkhani