Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akazi asanu ndi awiri adzagwira mwamuna mmodzi tsiku limenelo, nati, Ife tidzadya cakudya cathu cathu ndi kubvala zobvala zathu zathu; koma tichedwe dzina lako; cotsa citonzo cathu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 4

Onani Yesaya 4:1 nkhani