Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 37:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca kundikwiyira Ine kwako, ndi popeza kudzikweza kwako kwafika m'makutu mwanga. Ine ndidzaika mbedza yanga m'mphuno mwako, ndi capakamwa canga m'milomo yako, ndipo ndidzakubweza iwe m'njira yomwe unadzerayo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 37

Onani Yesaya 37:29 nkhani