Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 36:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, ukhulupirira ndodo yabango iyi yophwanyika, kunena Aigupto; imene munthu akaitsamira, idzalowa m'dzanja mwace, ndi kulipyoza; momwemo Farao, mfumu ya Aigupto, kwa onse amene amkhulupirira iye.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:6 nkhani