Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 35:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lidzaphuka mocuruka ndi kusangalala, ngakhale kukondwa ndi kuyimba; lidzapatsidwa ulemerero wa Lebano, ndi ukuru wa Karimeli ndi Saroni; anthuwo adzaona ulemerero wa Yehova, ukuru wace wa Mulungu wathu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 35

Onani Yesaya 35:2 nkhani