Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 34:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma bvuo ndi nungu zidzakhalamo, ndipo kadzidzi ndi khungubwi adzakhala m'menemo, ndipo Mulungu adzatambalika pamenepo cingwe coongolera ca cisokonezo, ndi cingwe colungamitsa ciriri cosatha kucita kanthu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 34

Onani Yesaya 34:11 nkhani