Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 31:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova atero kwa ine, Monga mkango, ndi mwana wa mkango wobangula pa nyama yace, sudzaopa mau a khamu la abusa oitanidwa kuupitikitsa, ngakhale kudzicepetsa wokha, cifukwa ca phokoso lao; motero Yehova wa makamu adzatsikira kumenyana nkhondo ku phiri la Ziyoni, ndi kucitunda kwace komwe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 31

Onani Yesaya 31:4 nkhani