Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye adzagumulapo, monga mbiya ya woumba isweka, ndi kuiswaiswa osaileka; ndipo sipadzapezedwa m'zigamphu zace phale lopalira moto pacoso, ngakhale lotungira madzi padziwe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:14 nkhani