Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka okhulupirira Aigupto. Tsoka kwa ana opanduka, ati Yehova, amene atenga uphungu koma si pa Ine; napangana pangano opanda mzimu wanga, kuti aonjezere cimo ndi cimo;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:1 nkhani