Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 3:25-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Amuna ako adzagwa ndi lupanga, ndi wamphamvu wako m'nkhondo.

26. Ndipo zipata zace zidzalira maiko; ndipo iye adzakhala bwinja, nadzakhala pansi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3