Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala m'malo mwa zotsekemera mudzakhala zobvunda; ndi m'malo mwa lamba cingwe; ndipo m'malo mwa tsitsi labwino dazi; m'malo mwa cobvala ca pacifuwa mpango waciguduli; zipsera m'malo mwa ukoma.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3

Onani Yesaya 3:24 nkhani