Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komanso Yehova ati, Cifukwa kuti ana akazi a Ziyoni angodzikuza atakweza makosi ao, ndi maso ao adama nayenda nanyang'ama poyenda pao naliza zigwinjiri za mapazi ao;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3

Onani Yesaya 3:16 nkhani