Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 29:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene apalamulitsa munthu mlandu, namchera msampha iye amene adzudzula pacipata, nambweza wolungama ndi cinthu cacabe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 29

Onani Yesaya 29:21 nkhani