Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 28:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa inu munati, Ife tapangana pangano ndi imfa, tabvomerezana ndi kunsi kwa manda; pakuti mliri wosefukira sudzatifikira ife; pakuti tayesa mabodza pothawirapo pathu, ndi kubisala m'zonyenga;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 28

Onani Yesaya 28:15 nkhani