Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 28:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka kwa korona wakunyada wa oledzera a Efraimu, ndi kwa duwa lakufota la ulemerero wace wokongola, limene liri pamutu paiwo, amene agwidwa ndi vinyo, m'cigwa ca nthaka yabwino.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 28

Onani Yesaya 28:1 nkhani