Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 27:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, mwa ici coipa ca Yakobo cidzafafanizidwa, ndipo ici ndi cipatso conse cakucotsa cimo lace; pamene iye adzayesa miyala yonse ya guwa la nsembe, ngati miyala yanjeresa yoswekasweka, zifanizo ndi mafano a dzuwa sizidzaukanso konse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 27

Onani Yesaya 27:9 nkhani