Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 27:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala tsiku limenelo, lipenga lalikuru lidzaombedwa; ndipo adzafika omwe akadatayika m'dziko la Asuri, ndi opitikitsidwa a m'dziko la Aigupto; ndipo adzapembedza Yehova m'phiri lopatulika la pa Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 27

Onani Yesaya 27:13 nkhani