Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 26:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo afa, atha, sadzakhalanso ndi moyo; ali mizimu, sadzauka; cifukwa cace Inu munawazonda, ndi kuwaononga, mwathetsa cikumbukiro cao conse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 26

Onani Yesaya 26:14 nkhani