Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye adzatambasula manja ace pakati pamenepo, monga wosambira atambasula manja ace posambira; koma Iye adzagwetsa pansi kunyada kwace, pamodzi ndi kunyenga kwa manja ace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:11 nkhani