Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, Inu ndinu Mulungu wanga, ndidzakukuzani Inu, ndidzatamanda dzina lanu, cifukwa mwacita zinthu zodabwitsa, ngakhale: zauphungu zakale, mokhulupirika ndi m'zoonadi.

2. Cifukwa Inu mwasandutsa mudzi muunda; mudzi walinga bwinja; nyumba ya alendo kuti isakhale mudzi; sudzamangidwa konse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25