Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova, Inu ndinu Mulungu wanga, ndidzakukuzani Inu, ndidzatamanda dzina lanu, cifukwa mwacita zinthu zodabwitsa, ngakhale: zauphungu zakale, mokhulupirika ndi m'zoonadi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:1 nkhani