Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 24:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace citemberero cadya dziko, ndi amene akhala m'menemo apezedwa ocimwa, cifukwa cace okhalamo a padziko atenthedwa, ndipo anthu owerengeka atsala.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 24

Onani Yesaya 24:6 nkhani