Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 24:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala monga ndi anthu, moteronso ndi ansembe; monga ndi mtumiki, moteronso ndi mbuyace; monga ndi mdzakazi, moteronso ndi mbuyace wamkazi; monga ndi wogula, moteronso ndi wogulitsa; monga ndi wobwereka, moteronso ndi wombwereka; monga ndi wotenga phindu, moteronso ndi wombwezera phindu kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 24

Onani Yesaya 24:2 nkhani