Malonda ace ndi mphotho yace zidzakhala zopatulikira Yehova; sizidzasungidwa kapena kuikidwa; cifukwa malonda ace adzakhala kwa iwo, amene akhala pamaso pa Yehova, kuti adye mokwana, nabvale caulemu.