Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala tsiku limenelo, kuti Turo adzaiwalika zaka makumi asanu ndi awiri, malinga ndi masiku a mfumu imodzi; zitapita zaka makumi asanu ndi ziwirizo, cidzakhala kwa Turo monga m'nyimbo ya mkazi wadama.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 23

Onani Yesaya 23:15 nkhani