Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 23:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katundu wa Turo.Kuwani, inu ngalawa za Tarisi; cifukwa wapasudwa, kulibenso nyumba, kulibe polowera; kucokera ku dziko la Kitimo kwabvumbulutsidwa kwa iwo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 23

Onani Yesaya 23:1 nkhani