Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Katundu wa cipululu ca kunyanja. Monga akabvumvulu a kumwela apitirira, kufumira kucipululu ku dziko loopsya.

2. Masomphenya obvuta aonetsedwa kwa ine; wogula malonda wonyenga amangonyenga, ndi wofunkha amangofunkha. Kwera Elamu iwe; zunguniza Media iwe; kuusa moyo kwace konse ndakutonthoza.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 21