Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 21:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace m'cuuno mwanga mwadzazidwa ndi zopota; zopweteka zandigwira ine monga zopweteka za mkazi pobala mwana; zowawa zindiweramitsa, makutu anga sangathe kumva; ndicita mantha sindingathe kuona.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 21

Onani Yesaya 21:3 nkhani