Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 20:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi imeneyo Yehova ananena ndi Yesaya, mwana wa Amozi, nati, Muka numasule ciguduli m'cuuno mwako, nucicotse, nubvule nsapato yako ku phazi lako. Ndipo iye anatero, nayenda marisece, ndi wopanda nsapato,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 20

Onani Yesaya 20:2 nkhani