Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye adzaweruza pakati pa akunja, adzadzudzula mitundu yambiri ya anthu; ndipo iwo adzasula malupanga ao akhale zolimira, ndi nthungo zao zikhale anangwape; mtundu sudzanyamula lupanga kumenyana ndi mtundu wina, ndipo sadzaphunziranso nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 2

Onani Yesaya 2:4 nkhani